Zzikukwa zisanu m’mziwiri zoyambirira zoti amayi ngoyera kudzodzedwa Unsembe
| Nchipangano Chakale anthu wakazi samawerengerenga ngati anthu monga anthu wamuna. Popeza amayi samkaumbala samawerengedwa ngati anthu osankhidwa ndi Mulungu. Choncho amayi analibe ufulu wopereka msembe zao paokha. Thawi zonse ntchito zao pa zachipembedzo zimakhala zongothandiza amuna omwe ankawapondereza. | ![]() |
![]() | Ambuye Yesu anasudzula nchitidwe wopondreza amayi |
Zina? |
1 | 2 | 3 | 4 | 5 | 6 | 7 |
obatizidwa | olimbikitsidwa | omasulidwa | odzodzedwa | ovomerezedwa | othandizika | oitanidwa |


