Zoonadi, kalelo Mpingo unkakana kudzodza amayi kuti akhale ansembe. | ![]() |
![]() | Mfundo zitatu zopondereza zimalepheretsa amayi kutumikira muunsembe. 1. 1. Amayi ankaonebwa ngati otsalira mu zonse: mphamvu za thupi, mu mzeru ndi mu kulimba mtima. 2. Popeza Eva adagwetsa mtundu wa anthu, mkazi aliyense ankaganiziridwa kuti ali ndi themebrero la Eva. 3. Anthu amaganiza kuti mayi akakhala akasamba ndiye kuti ndiwodetsedwa.
|
Nthawi zonse Mpingo usowa kudzimasula mu mtcichidwe wa tsankho womwe umaonengwa ziphunzitso ndi zizolewezi zabwino mu mpingo.
Amayi a lero ayenera kumasulidwa mu la chimpunzitso cha tsankho mu mpingo chomwe chimaletsa amayi kutenga mbali mu utumiki wa unsembe umene Mulungu adawaitainira. | ||
Zina |
1 | 2 | 3 | 4 | 5 | 6 | 7 |
obatizidwa | olimbikitsidwa | omasulidwa | odzodzedwa | ovomerezedwa | othandizidwa | oitanidwa |


