| tikatsatiza mbiri ya MpingoIn the course of the Church’s history, ntchito zitatu za utumiki zasanduka ntchito zomwe anthu okhaokha odzodzedwa amagwira . Izi mzomwe nthawi zina zimadziwika ndikuti sacramenti la unsembe. Mchikatolika tikuzidziwa ngati u episikopi, unsembe ndi udikoni. Ngakhale kuti ma udindo ngosiyana, ntcito zitatu zonsezi nzogwiranaThough different in scope, all three are part of musakramenti limodzi la ukulu mu unsembe.
| ![]() |
![]() | A mayi anankadzodzedwa u dikoni pa chiyambi cha mpingo. Za mchitidwewu Ma dikoin a akazi anali ofunika Women deacons assisted Tikudzewa za mwambo weniweni womwe ankatsatiza podzodza amayi. A Bishopi ankawasanja manja pa mutu ndipo ankapempha Mzimu Woyera kuti awatsikire ndi madalitso ndiponso ankawaveka sitolo ya u dikoni khosi mwawo. Padalibe kusiyana pa kudzodzedwa u dikoni kwa a mayi ndi abanmbo popeza anali ndi utumiki wofanana.
|
Chigawo cha ku m’mawa cha mpingo wa Katolika pa nthawiyo chinali monnga ulili Mpingo wa Katolika popeza kugawikana (Eastern Rite) kudabwera mchaka cha 1054.. Ngati amayi ankalandira Sacramenti la Unsembe pa nethawi imeneyo, alakeranji kudzodwa nthwi zino. | |||
![]() Buku lo kamaba za u dikoni wa amayi lomwe lasindikizidwa posachedwapa “Ili ndi buku lolebwedwa mwa luso lomwe latsatiza mbiri ya mpingo mozama ndipo mogwira mtima, lolembedwa ndi mlembi yemwe amadziwa nkhawa zomwe akhristu alinazo mu mtima polingalira mtsankho lomwe limatchingiriza amayi kulowa unsembe . A Wijngaards agwiranso ntchito yapamwamba potanthauzira makalata akale omwe munalembedwa mbiri ya mpingo kuti anthu onse athe wodziwerengera paokha.”
Reviews —– * —– How to Order | |||
Zina? | |||
1 | 2 | 3 | 4 | 5 | 6 | 7 |
Kubatizidwa | Kulimbikitsidwa | Kumasulidwa | Kudzodedwa | Kuvomerezedwa | Kuthandizidwa | Kuitanidwa |



