Nkhani ya ufulu wokhala mayi?

“Nkhani yeniyeni apa ndi ufulu wokhala mayi.

Amayi masiku ano awirikiza pankhani ya yopitsa mtsogolo ufulu wokhala mayi pakati pa magulu omwe apanga tsankho ndi anthu a akazi! Izi nzofunika makaka ku ntchito, koma osati ku tchalitchi!”

“Pepani, anzanga!

Nkhani ya ufulu ya amayi ndi yofunuika kwambiri mu mpingo . Kuti mpingo uyende bwino ndi kutukuka nkhaniyi tiyiganizire mozama ndi mwachilungamo!

Mzoonani kuti nkhondo ya amayi pomenyera ufulu wawo ya tithandiza amayi kundikira kuti amainso ali ndi gawo lofunika mu ntchito za mpingo. Nkhondoyi si yachilendo popoza maziko ake ali mu mbiri ya mpingo.”

Nzachisoni kuti Tchalitchi chinatengera chikhalidwe cha mitundu yambiri yomwe imatenga amayi ngati anthu operewedwa mu umunthu wawo!

“INU AMAYI mufuna kusintha chiphunzitso cha mpinzo ncholinga choti zinthu zizikukomera mbali yanu .

Koma ife tisankha kutsatiza chimphunzitso choyera cha mpingo chomwe sichisintha.

Thalitchi silingasinthe malumulo ake kuti liwoneke lotukuka kapena kukondweretsa amayi omwe afuna kufanana ndi anthu amuna!”

“Kulakwa!

Ayi, sitisowa kusintha malamulo a mpingo.
Chomwe chisowa kusintha ndi maphunziro ena a mpingo amene amakuza chizolowezi cha tsankho lopondereza amayi.

Tiyenera kuchotsa mfundo zonse zimene zimaika khungu m’maso mwa atsogoleri a mpingo amene amatanthauzira chiphunzitso cha mpingo mokondera popondereza amayi. Izi zimabweretsa khungu lomwe likutilepheretsa kumvetsa tanthauzo lenileni la Malembo Woyera.

Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi uphunzitsi wa mpingo wa mtsankhoMafunso apafupipafupiZina?
kusintha kwa chikalidwemfundombirikumvera kwenikweninthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi?uphunzitsi wosatsutsika?kudalilika?kumvera?kederera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mtchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?