| Maziko a mkuitanidwa ku moyo uliwonse ali amafumira moti tinalenngedwa ndi Mulungu. Mphatso zathu zonse timalandira kuchokera m’manja mwa Mulungu chomwechonso kuitanidwa kwathu, kaya mkuntchito, ku utumiki kapenaso ku ntchito yokatumikira mafuko ena, zonsensi zimatheka popeza Mulungu amatiitana ife amene sitinali kathu mkomwe potisandutsa ana a Mulungu.
| ![]() |
![]() | Ponena mwa mosapsyatira pali umboni woti amayi ambiri a Chikatolika, mziko lonse lapansi, amagundidwa mu mtima kuti Mulungu akuwaitanira ku unsembe. Werengani Kalero kuitanidwa kwa amayi ku unsembe, nthawi zambiri, kumatchingirizidwa ndi chikhalidwe cha tsankho cha mafuko a anthu. Ngakhale zinali cnoncho, tili ndi zitsanzo za mbiri za amayi Woyera amene anavomera kuitanidwa ku utumukiwu: Zotsatira za kafukufuku ofufuza maganizo a amayi 100 omwe anamva kuitainidwa ku unsembe m’mitima mwawo zikusonyeza kuti amayiwa ali ndi luntha, ndi wodzipereka ndiponso woyenera unsembe monga amuna onse amene amamva kuitananidwaku Werengani pano. |
Kudzera mu kugunda mu mtima mwa amayi a Chikatolika omwe ndi oyinanidwa ku kuunsemmbe Mzimu Woyera ukupempha Mpingo kuti uwunikirenso pa za mtsankho lomwe limalepheretsa amayi kulowa unsembe.
Mu mpingo mpaka padzakhale kusintha tikapanda kumva kugunda kwa Mzimu Woyera mtimima ya amayi, ntchito za mpingo zimanidwa mphatso za mtengo wapatali zomwe Mzimu Woyera wapereka kwa Amayi. | ||
Return to preasons |
1 | 2 | 3 | 4 | 5 | 6 | 7 |
obatizidwa | olimbikidwa | omasulidwa | odzodzedwa | ovomerezedwa | othandizidwa | oyitanidwa |


