| “Kuchokera ku maymbiriro enieni a mbiri ya mpingo mpaka nthawi zino, chikonzero cha Mpingo chinali choletsa kudzodza amayi sakramenti la unsembe.” | ![]() Bungwe la Aphunzitsi akulu a Mpingo | “Zoonadi, Amayi amatumikira mu nchtito zina zofunika mu Mpingo, koma mwa ntchito zonszi padalibe zokhudzana ndi ntchito za odzodzedwa unsembe.” Commentary on Inter Insigniores § 57, 71-77. |
| Kupatura zitsanzo zingapo zopatulika, , amayi samkadzodzedwa unsembe. Zikomo!
Amayi ankaganirizidwa kuti : | Chonde, werengani nfundo! | |
![]() | Ngakhale panali makhalidwe a tsankho lopondereza amayi, a Khristu akhala ndi nthumazi yoti akazi ndi amuna ndi anthu ofanana kudzera mchipulumutso cha Khristu. Amadziwanso, pansi pa mtima, kuti amayiangathenso kukhala asembe abwino. Zoterezi timazitcha chikhalidwe cha tsankho chomwe chimasowa otsutsa Zitsanzo zina za zizolowezi kuwalemekeza mupitiriza muyezo ‘Le sacerdoce de la Vierge’ (close up), early 15th century, school of Amiens, France. | |
| Poonjerara apo, pa zaka pafupifupi 900 Mpingo umalora ami kutumikira mu ntchito za unsembe pomwe umadzadza amayi ngati ma Dikoni Pa za Mwambo odzodza ansembe, womwe amkasanjika dzanja la manja pamutu ndi kupempha Mzimu woyera kuti atsikire pa odzodzedwa, padalibwe kusiyanitsa pakati pa abambo ndi amayi. Ngakhalenso Amayi amadzodza ndi kulandira mphamvu zonse za utumiki wa u Dikoni kudzera mu sakramenti la u Dikoni Choncho, chizolowezi si chifukwa chokwanira kuti tidzichita ntsankho kwa amayi pa utumiki wa Unsembe. | ![]() Zina |



Chonde, werengani nfundo!

