Tikayanira za mbiri ya Mpingo, Akatolika ambiri amaopa kukamba za ufulu wa akhristu mu tchalitchi chathu. Iwowa amaganiza kuti kukamba za ufulu wawo zitha kusiyana ndi maganizo a akukuluakulu kapenaso kuti kutereko mkusamvera Malamulo a Mulungu. Zoona zenizeni mzakuti pali zifukwa zomweka bwino zoti anthu athetse mantha amenewa ndi kuyamba kukambirana za ufulu weniweni wa akhristu.

Pano tinene mosabisa kuti tiri ndi maufulu, poyamba ngati anthu wolengenga ndi Mulungu ndiponso ngati mamembala a Tchalitchi.
*Ambuye Yesu anatipatsa mphamvuyosanduka ana a Mulungu (John 1,12). moga ana a amuna ndi a akazi,ndipo ngati athu wosankhidwa, tili ndi maufulu ambiri amene Mulungu anatipatsa (Romans 8,17).
* Ngakhalenso akuku a Mpingo mpaka lero kawirikawiri makamba za “maufulu” a mamembala a mpingo: pali ndime 26 mu Malamulo a Tchalitchi otchedwa Canon Law okamba za ufulu wa akhristu eniake. (can. 204 – 231).
* Thchalitchi lisowa kusintha mwachangu mu mfundo ndi njira zomwe athogoleri akuyendetsera mpingowu maka pa nkhani za ufulu wa anthu. Maufulu a akhristu, ansembe ndi mabishopi, amaene ndi mphtso zochekera kwa Mulungu akupondrezedwa mu dongosolo loyendetsera mpingo lomwe tilinalo panoli!
Choncho ife tikukupepha inu nonse awerengi athu kuku mutithandize polimbitsa We therefore urge our visitors to give full cooperation and allegiance to the Bungwe lokwenza ma “Ufulu a Akatolika mu Tchalitchi” (arccsites.org) Bungweli la lemba makala awiri omwe akupereka maganiozo ozama pa za ufulu wa akhristu:
Three afterthoughts:
1. Mtchalitchi cholemekekeza ,In a perfect Church, sitisowa kupondereza ufulu wa akhristu , monga mu ukwati wolemekeza nkhani ya ‘maufulu’ a bambo ndi mayi siikhal nkhani ya makangano.Komano, mongo BUngwe loyanira malamulo a Tchalitch limatiphunzitsa, Tchalitchi chathu “chimasowa kusintha” nthawi ndi nthawi. (Vatican II, Ecumenism § 6). Izinso nzofunuika kwambiri nthawi yathu ino pamene nkhanza za anthu ena amene ali ndi udindo mtchalitchi zikupangitsa kuti tchalitchi chathu chiwomeke nga ‘banja losowa chilungamo ndi mtendere”.
2. Timamva kawirikawiri ku ‘Mu Tchalitchi mulibe Demokalase’. Zinthu siziyenera kukhala choncho. Titha kunena kuti si Demokalase tialingalira kuti Mpingo udayambika mchifuniro cha ambuye yesu osati kubzolera mu voti ya wanthu. The Church is not a democracy in the sense that it was founded by the will of Christ, not by a plebiscite. Komano izi sizitanthuza kuti mu utsogoleri wa Mpingo uzisiyana ndi chifuniro cha anthu, Demokalase ndi njira yolamulira mpingo omwe igwirizana ndi chitukuko cha makono osati ulamuliro wachikale omwe mafumu paokha amamanga mfundo zoti athu wamba atsatitire..
3. Papa Paul VI anaitanitsa anthu kuti apange Bungwe lounikira Malamuro a Mpingo ndi kulemba Buku la malaumulo a Mpingo loti litsogoze a Khristu. Mzchisoni kuti pambuo pake maganizo oyamikikawa sanatsatidwe.
