![]() | “Malakhulidwe anu, akuchepetsa chikhulupiro changa mwa bamphunzitsi a Mpingo!Popeza kuti a Mpunzitsi ena a Mpingo akhala akuganiaza molakwika pa zambiri m’mbuyomu, tingadzakhalenso bwanji ndi chikhulupiriro mwa a Phunzitsiwa.!?” |
“Mzoonadi!A Mphunzitsi a Mpingo ali ndi udindo wofunika mu Tchalitchi. Titha kufananitsa ndi udindo wa mabungwe woyanira zakudya ndi umoyo wa anthu womwe ali ndi ntchito yowonetsetsa kuti anthu akahale ndi umoyo wa ngwiro ndi thanzi. Choncho sisikutithandiza mu Mpingo wathu tikamaona kuti a Khristu akutaya ayamba kupeneka mu chikhulipirio chomwe amayika pa atsogoleri a Mpingo, izi zikuchiku chifukwa a Phunzitsi Mpingo anataya, ndipo adakatayiratayira kudalilika kwawo pa za uphunzitsi. Tchalitchi chathu chisamaiwale mau a Khristu amene amakamba za mchere womwe wataya kukoma kwake. | ![]() |
![]() | “Mchere wotaya kukma kwake?Mukutanthauzanji?” |
“Kuti anthu akhalenso pa chiphunzitso cha Mpingo, ku Vatican, likulu la Mpingo liyenera kulekeratu zizolowezi zosathandiza monga:
| ![]() |




