Kodi tingaikenso chikhulupiriro chathu mwa a Phunzitsi a Mpingo?

“Malakhulidwe anu, akuchepetsa chikhulupiro changa mwa bamphunzitsi a Mpingo!

Popeza kuti a Mpunzitsi ena a Mpingo akhala akuganiaza molakwika pa zambiri m’mbuyomu, tingadzakhalenso bwanji ndi chikhulupiriro mwa a Phunzitsiwa.!?”

“Mzoonadi!

A Mphunzitsi a Mpingo ali ndi udindo wofunika mu Tchalitchi. Titha kufananitsa ndi udindo wa mabungwe woyanira zakudya ndi umoyo wa anthu womwe ali ndi ntchito yowonetsetsa kuti anthu akahale ndi umoyo wa ngwiro ndi thanzi.

Choncho sisikutithandiza mu Mpingo wathu tikamaona kuti a Khristu akutaya ayamba kupeneka mu chikhulipirio chomwe amayika pa atsogoleri a Mpingo, izi zikuchiku chifukwa a Phunzitsi Mpingo anataya, ndipo adakatayiratayira kudalilika kwawo pa za uphunzitsi.

Tchalitchi chathu chisamaiwale mau a Khristu amene amakamba za mchere womwe wataya kukoma kwake.

“Mchere wotaya kukma kwake?

Mukutanthauzanji?”

“Kuti anthu akhalenso pa chiphunzitso cha Mpingo, ku Vatican, likulu la Mpingo liyenera kulekeratu zizolowezi zosathandiza monga:

  • Kutsekereza Bungwe la ma Bishopi pa pomwe ali kumbirana mwaufulu wawo pankhani za Mpingo.
    Sinodi ya ma Bishopi inayambika ndi mfundo za pa nsonkhano wachiwiri wa Vatikani kuti mabishopi akahlenso ndi mphmvu zounikanso mfundo za Khanso yayikulu yotchedwa ‘Curia’.
  • Kulowerera pomwe ma Bungwe a aBishopi akugwira ntchito za udindo wawo mwadongosolo.
    Tikudziwanso kuti ma Bishopi si akazembe a aPapa koma ndi akazembe a Khristu, choncho ayenera kugwira nchito yawo ya ukazembe popanda kusokonedwa ndi akulikulu ku Vatikani.
  • Kusankha anthu amantha omwe satsutsa zolakwika za kulikulu kuti akhale a Bishopi, nthumwi za ku mabungwe a akatswiri ophunzira za Mulungu ndi anthu ena kuti alowe m’maudindo ofunika mu Mpingo.
    Zimenezi zimapangitsa kuti Tchalitchi likhale ndi atsogoleri amene sangathe kutsata maganizo awo abwino mopanda mantha, koma omwe amangovomereza zomwe akulu ena akuwauza.
  • Kupondereza akatswiri ophunzira ntchito za Mulungu omwe amatsutsa atsogoleri akulu akapereka maganizo olakwika.
    Kuponnderezana kotereku kukupha luntha la atsogoleri ambiri ameme amaganiza mwanzeru, mozama komanso mopanda chinyengo.”
Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi a Phunzitsi a MpingoMafunso apafupipafupiZina?
Kusintha kwa chikhalidwemfundombirikumvera kwenikwenimnthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi?uphunzitsi wa mpingo wosatsutsika?kudalilika?kumvera?kuderera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mu Tchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?