![]() | “Zoonadi!Bungwe akatswiri pa Chiphunzitso cha chikhulupiriro chathu lagamula kuti nkhani ya unsembe wa amayi ndi chiphunzitso chosasinthika!!!a Kadinolo Ratzinger, Mtsogoleri wolamulira Bungwe la akatswiri pa za Malamulo woyera a Mpingo anati: ‘nkhani zokambirana unsembe wa amayi zamangika popeza nkhaniyi yalowa mu ziphunzitso zosatsuka za mpingo kudzera nchilamulo cha Aphunzitsi akulu a Mpingo. ” |
“Anaterodi? Kuletsa nkhayini, komadi?A ‘Phunzitsi akulu a Mpingo a dziko lonse la pansi’ amayimira chiphunzitso ndi maganizo a ma Bishopi onse a Dziko la pansi. Komano a Bishopi onse pamodzi sanagwirizanepo chiphunzitso chioletsa kupitiriza kukambirana unsembe wa Amayi.” | ![]() |
![]() | “Tayambani mwaima kaye!Pali unyinji ma Bishopi a dziko la pansi omwe amakhulupirira kuti amayi sangadzodzedwe unsembe. Izi nzachidziwikire chifukwa ambiri mwa ma Bishopiwa anasankhidwa chifukwa amagwirizana ndi maganizo a Papa pa nkhani ya unsembe wa Amayi!” |
“Tiyeni tiunikirenso nkhaniyi!Mkutheka kuti mabishopi onse a dziko la pansi amakhupirira kuti amayi siwoyenera kulowa unsembe. Chigwirizano choterechi chimaziwika ndi mau akuti opinio communis (maganizo ogwirizana). Opinio communis Komano poyang’anira mbiri ya Mpingo tiona kuti chigwirizano cha maganizo a ma Bishopi chithanso kukhala ndi zolakwika. Zaka 100 zapitazo ma bishopi ambiri amatsutsa maphunziro a Sayansi omwe amalongosola za mayambiriro a chilengedwe cha anthu. Nthawi imeneyo panali chikhupiriro chozama choti dziko linalenedwa m’masiku asanu ndi limodzi! Izi sizikutanthauza kuti ma Bishopi onse umagwirizana pa umphunzitsi umenewu. | ![]() |
![]() | “Nanga chimapangitsa kuti nkhani ikhale uphunzitsi wa ma Bishopi mogwirizana wogwizana ndi chiyani?Kodi nsonkhano waukulu wachiri ku Vatikani sudagwirizana kuti: ‘Ma Bishopi, pamozdi ndi a Papa, monga a phunzitsi akulu mu Mpingo ayenera kulemekezedwa ndi aKhristu onse monga atetezi achifuniro cha Mulungu mu tchalitchi la Katolika? |
“Chabwio, tiyeni tiwerengwe ndime yonse ya nkhaniyi!Nsonkhano wachiwitri ku Vatikani udati: ‘ Ma Bishops angathe kulamula kuti maphunziro Khristu ndi wosatsutsika, nthawi ina iliyonse pomwe, ngakhale atakhala malo osasiyansiyana, pokhapokhapo ngati maganizo awo ngogwirizana ndi maganizo a Papa, ndipo maBishopi onsewa pamodzi ngati agwirizana kupereka uphunzitsi wowona pa za chikhulupiriro ndi umunthu. Ndipo payenera kukhala chigwirizano chopanda kukaika pa mfundo zomwe amanga limodzi. ’ Pali mfundo zisanu zoyeneretsa chigwirizanochi:
Tikaunika pa nkhani ya unsembe wa amayi tiwona kuti nkhanii yatsekedwa mosatsatira dongosolo limeneli!” | ![]()
|
![]() | “Inu ma Bishopi mwavomereza magazizo ndi Kadinolo Ratzinger?!Maganizo amenewa mwawatenga pa maphunzitso ati mu mpingo wathu?!” |
![]() |











