![]() | “Ena akuti tikuderera a atsogoleri a Tchalitchi popereka maganizo athu atsutsa tsankho loretsa amayi kulowa unsembe!akuti zomwe tikulembazi mzosokeneza athu wamba omwe sanazambe pa uphunzitsi wa Mpingo! Suja Ambuye Yesu anati yemwe achita zochititsa manyazi pa gulu la ana amakwingiridwe chimwala chlemera m’khosi mwake ndipo aponyedwe mnyanja yozama!” (Matthew 18,6) |
“Mungakhulupirire izi!Anthu ambiri omwe amkalemekeza mafumu anaphedwa chifukwa cholimba mtima potsutsa zolakwika zina, nzachisoni kuti upandu woterewu umachitikanso mu Tchalitchi chathu. pambuyo pa zonsezi Mpingo umadzionongera mbiri yake yabwino.” | ![]() |
![]() | “Tithana ndi onse wotsutsa!Tikuti, dziwaponyani m’nyanja anthu otsutsa onsewo. Kuti mpingo wathu upite patsogolo, tisawamvere chisoni anthu otsutsana nafe, tithane nawo basi!” |
“Kumeneku ndiye kumanga Mpingo, eti?Taimani mkukambire kankhani! Pa Okotobala 22, 1707, mkulu wa gulu la ankhondo a panja ,Clowdesley Shovell, anabwere ku England pambuyo pa nkhondo omwe anamwnyana ndi amwaliwongo. Iwowa anali ndi sitima za pamanyanja zisanu pa nyanja ya Mediterranean. | ![]() |
![]() |





