Maphunzitso a Mpingo omwe amadzetsa tsankho lomwe limatchingiriza Amayi kutenga mbali mu utumiki wa unsembe amatsutsana ndi Malembo Woyera, chikhalidwe cha Mpingo ndi maphunzitso a za Mulumgu.

Zokhumudwitsa mzakuti mkoletsedwa kukambirananso mfundo zomwe zimabweretsa tsankho lotchingiriza Amayi ku unsembe. Akulu akulu woyang’ira maphunzitso a Mpingo a akupondereza ufulu wa Amayi..

Mukafuna kuziwa zambiri za zomwe tikutsutsa mpingo pa nkhaniyi, werengani zomwe tatonkha pa za maganizo a anthu osiyanasiyana.

Pano tikamba Mfundo zina mosabisa.

1. Ambuye Yesu anapereka kwa Amai gawo la utumki chimodzimodi ndi abambo

ndinso

anawalimbiotsa powapatsa Amayi, monga bambo, mphamvu zosandulitsa Ukalistia,.



 
 

2. Until at Kwa zaka 900 .
Mpingo unadzodza
zikwi zikwi za Amayi mu utumiki
wopereka mkate monga a Dikoni.


3. Kudzera muubatizo wawo, amayi monga abambo, amasanduka kukhala ana a Mulungu..

Mphatso ya ubatizoyi imayeneretsa, amayi monganso abambo, kulandira ma sakramenti onse ndipo ngakhale kudzodzedwa ku unsembe.

“Komadi ku Roma analamula kuti nkhaniyi nchimphunzitso chomwe a Khritsu alibe mphamvu zotsutsa?!”

Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi uphunzitsi wa mpingo wa mtsankhoMafunso apafupipafupiZina?
kusintha kwa chikalidwemfundombirikumvera kwenikweninthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi?uphunzitsi wosatsutsika?kudalilika?kumvera?kederera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mtchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?